Zina Zokhudza nkhondo

1 year ago
4

Mfundo zambiri zokhuza mikangano ya m zidanenedwa pa Novembara 12, 2022, pa msonkhano wa pa intaneti "Mavuto a Padziko Lonse. Kupulumuka Kwathu kuli mu mgwirizano." Kwa nthawi yoyamba dziko lapansi lidamva chowonadi chodabwitsa chokhudza consumerist fomati yomwe takhalamo mzaka 6 000 zapitazi.

Muvidiyoyi muphunziramo:

➡️ Takhala masiku angati popanda nkhondo?

➡️ Ndi anthu angati omwe atayika pa mikangano ?

➡️ Cholinga chachikulu cha consumerist fomati chomwe chikuwononga miyoyo yathu ndi chiyani?
➡️ Mfundo 10 zopangira nkhondo

Tsopano tikuzindikira kuti chikhalidwe chamakono cha anthu chafika pachimake cha kudziwononga tokha. Kulakalaka mphamvu ndi phindu kumaposa nzeru. Palibe amene amakhulupirira wina aliyense. Talowa m'nthawi yamavuto apadziko lonse lapansi. Koma lero ndi pamene tingathe kusintha zinthu. Kuti tichite izi, ndikofunikira kusintha chikhalidwe, ndiko kupita ku dziko lokomera aliyese, momwe moyo wamunthu udzakhala wamtengo wapatali kwambiri.
Uwu ndi mwayi wathu wokhawo wopulumutsa anthu ku chiwonongeko.

🌏 Msonkhano Wapadziko Lonse Wapaintaneti "Zovuta Zapadziko Lonse. Kupulumuka kwathu kuli mu mgwilizano" ndikusankha zilankhulo:
https://creativesociety.com/global-crisis-our-survival-is-in-unity

⏩ The Foramu mu English:

https://youtu.be/vPcyhZcDDXs

⏩ Mavuto a Padziko Lonse. USA | Msonkhano Wapadziko Lonse Wapaintaneti, Sepitembara 24, 2022:
https://www.youtube.com/watch?v=SeJR_KPWXrw&t=2s

⏩ Kanema "mavuto a kusintha kwa nyengo":

https://www.youtube.com/watch?v=YcOerQhv3_I

💠 Tsamba lovomerezeka la Creative Society polojekiti ya pa intaneti

https://creativesociety.com

📩 Imelo:info@creativesociety.com

▶️ Twitter: https://twitter.com/CreativeScty?t=ppbfpAOO1CR1dXrJNPhaAw&s=09

▶️ Facebook:/https://www.facebook.com/CreativeSociety.en/

▶️ Instagram:https://www.instagram.com/creativesociety.official.en/

#CreativeSociety
#mavuto a dziko lonse
#mikangano
#mtendere
#moyobamba

Loading comments...