Dziwani za Creative Society: Dziko Lamaloto Anu

1 year ago
4

🌏Onani zotsatira za kafukufuku wapadziko lonse wopangidwa ndi Creative Society , kunena zoonadi zomwe anthu amafuna.Onelani pamene anthu ma miliyoni odzipereka kuchokera mu mayiko 180 akugawana masomphenya awo a moyo wamtendere, wotetezeka komaso wachimwemwe. Tsono phuzirani mizati 8 Ya creative society imene imafotokoza kukwanilitsa zokhumba za anthu 100%.Kuyambira ufulu komaso chitetetezo, kupanga zinthu mosabisa komaso dziko lolamulidwa ndi anthu. Kanema otsatirayu akufotokoza mmene Creative Society idzakwanilitsire maloto anu. Tiyeni titengepo mbali pofalitsa uthengawu kuti masomphenya athu akwanilitsidwe.

🤝 Lowani tsopano! Khalani otenga nawo mbali pantchito yomanga gulu latsopano logwirizana la Creative, komwe Moyo wamunthu ndi wamtengo wapatali kwambiri!

🌏Dziwani zambiri pa msonkhano wa pa intaneti "Mavuto a Dziko lonse. Pali njira yothetsera mavutowa” kumasulida mu m’zinenero 150!

➡️https://www.youtube.com/live/klpZyZdWTrs?feature=share

➡️ Nthawi ikutha. Chochitika chachikulu kwambiri m'mbiri: https://youtu.be/dvy5wNNiIxc
➡️ Msonkhano Wapadziko Lonse "Zovuta Zapadziko Lonse. Kupulumuka Kwathu Kuli mu Umodzi" ndikusankha zilankhulo: https://creativesociety.com/global-crisis-our-survival-is-in-unity

▶️ Onerani Msonkhanowo mu Chichewa:
https://youtu.be/slMKTTZjI7E

➡️ "Ubwino kwa Munthu mu Creative Society": https://youtu.be/v5notckMY3Q

➡️ Tsamba lovomerezeka
ndi polojekiti ya Creative Society.
https://creativesociety.com

📩 Imelo: info@creativesociety.com

▶️ Lowani nawo gulu la anthu odzipereka a polojekiti ya Creative Society:
https://creativesociety.com/join-us

▶️ Lembetsani ku Telegraph Channel yathu ndikukhalabe ndi zochitika zamakono:
https://t.me/creativesociety_en

▶️ Twitter: https://twitter.com/CreativeSct

▶️ Facebook: https://www.facebook.com/CreativeSociety.project

▶️ Instagram: https://www.instagram.com/creativesociety.official/

#CreativeSociety
#GlobalCrisis
#ThereIsWayOut

Loading comments...