VOSKHOD MPC mu Dziko

1 year ago
24

Ngakhale voskhod Mpc idapangidwira nthawi yosinthira kuchoka mu consumerist format kupita mu Creative Society. Ikhoza kugwiritsida ntchitoso pa dziko kapena pa mayiko amabiri komaso mu consumer society.Mu consumerist Format , ufulu pa nkhani imapeleka mafuso ambiri chifukwa imayika dziko pa mavuto ambiri.Potengera chimenechi, kagwilitside ntchito ka VOsKhod MPC mu dziko imayenera kugwilitsidwa ntchito mosamala komaso pasi pa mtsogoleri wa dziko.
Ubwino Pazachuma mu dziko
Mu nkhani ya za chuma, voskhod mpc imapangitsa boma kukhala lotetezeka ku mayiko ena.Iyi imathandiza kukoza mitengo , kuchuilukitsa ma polofeti pounikila bwino nkhani ya zachuma. Imapititsa patsogolo nkhani ya zachuma komaso moyo wa anthu.Izi zimapereka chilimbikitso komaso kudalilika kwa boma.
Titati tiyike ubwino wa Voskhod MPC ku dziko : Kupititsa patsogolo kapangidwe ka bajeti koyenera, kukweza moyo wa anthu,Kukozaso kayendetsedwe ka dziko, United States itha kuseva 2.5 tililiyoni ya ma dollazi pa bajeti yawo ya pachaka
Itatha kuona mmadera ose a kayendetsedwe ka dziko,Voskhod MPC imatha kulosera moyenera mmene chuma chingayendere.Izi zimapangitsa kuti ndalama ziikidweso mu ma kampane, ndi ma indasitile zomwe zigwile ntchito moyenera mu dziko lovuta ndalamali ndikulosera ma polofeti ochuluka.

Loading comments...